Universal Declaration of Human Rights - Nyanja/Chinyanja
Content Category
Nyanja/Chinyanja
CHIBVOMEREZO CA LAMULO LOSAMALIRA KHALIDWE LA MUNTHU PA DZIKO LONSE LA PANSI CIYAMBI Popeza kuti citsimikizo ca khalidwe loyenera la munthu mu banja lonse ndico tsinde la ufulu, ungwiro ndi mtendere...